Mmh-mmh (eni pandova)
Ay-yah-yah-yah-yah
(Njuchi) eti monga sudziwa?
(Sudziwa iwe!)
Sine chithumwa
Sine kanyanga
Zondibisa ngati ndondocha
Nono ndakanana
Babe monga sumadziwa?
Pali ma emotion wa
Ndayesa kuwapewa
Koma zikumandiwawa, ah
Umangopempha ma photo
Koma sumawa poster ma photo
Ine zomandibisa nono
Sindine kathumba kachamba
Timawakamba makolo
Koma samandidziwa makolo
Ine zomandibisa nono
Sindine kathumba kachamba
Sine kathumba
Sine kathumba
Sine kathumba
Sindine kathumba kachamba, nono
Sine kathumba
Sine kathumbaa
Sine kathumba
(sindine kathumba kachamba)
Sine chithumwa
Sine kanyanga
Zondibisa ngati danzi, nono ndakana
Mundidziwitse, mwina ndimakupangitsa manyanzi
Sindili single ineyo
Tikamayenda dzanja udzindi holder ine
Ine si business
Ine si business ya illegal hunnie
Mwina pali ena, mwina pali ena, hunnie
Ine ndi sweetness
Pandekha ndine thumba la illovo hane
Mwina pali ena
Mwina muli ndi ena hane
Kumandi poster ma photo
Mam'mawa, masana, madzulo
Zomandibisa nono
Sindine kathumba kachamba
Akandione anzako
Adziwe uli ndika girl
Zomandibisa nono
Sindine kathumba kachamba (eeh-eeh)
Sine kathumba (eeh-eeh)
Sine kathumbaa
Sine kathumba
Sindine kathumba kachamba, nono
Sine kathumba
Sine kathumbaa
Sine kathumba
Sindine kathumba kachamba
Sine kathumba
Sine kathumba
Sine kathumba
Sindine kathumba kachamba, nono
Sine kathumba
Sine kathumba
Sine kathumba
Sindine kathumba kachamba
Mmh-mmh
Mmh-mmh
Mmh